Tseketseke a Laz abwera

Lazalo muliyenda Atakhala kunja kwa Mwezi, kuombedwa mphepo zina mmizinda ya ku Kenya, America ndi UAE, mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera afika kumudzi tsopano. Ndipo abwela ndi chithumba chimene chikuyembekezereka kuthetsa mavuto a kusowa kwa mafuta, kuzimazima kwa magetsi ndi chipwirikiti pa za chuma. A Chakwera anachoka ku Malawi pa 12 Mwezi watha […]

Tseketseke a Laz abwera

Leave a comment

Design a site like this with WordPress.com
Get started